Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 10:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anali nao ana amuna makumi atatu okwera pa ana a aburu makumi atatu, iwo ndipo anali nayo midzi makumi atatu, ochedwa midzi ya Yairi, mpaka lero lino, ndiyo m'dziko la Gileadi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 10

Onani Oweruza 10:4 nkhani