Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yuda ananena ndi Simeoni mkuru wace, Kwera nane ku gawo langa kuti tiwathire nkhondo Akanani; ndipo inenso ndidzamuka nawe ku gawo lako. Namuka naye Simeoni.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:3 nkhani