Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 1:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Manase sanaingitsa a ku Betiseani ndi midzi yace kapena a Taanaki ndi midzi yace, kapena nzika za ku Dori ndi midzi yace, kapena nzika za ku Ibleamu ndi midzi yace, kapena nzika za ku Megido ndi midzi yace; koma Akanani anakhumba kukhala m'dziko muja.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:27 nkhani