Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Mkeni mlamu wace wa Mose, anakwera kuturuka m'mudzi wa m'migwalangwa pamodzi ndi ana a Yuda, nalowa m'cipululu ca Yuda cokhala kumwela kwa Aradi; namuka iwo nakhala ndi anthuwo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:16 nkhani