Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Obadiya 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu onse a akupangana nawe anakuperekeza mpaka pamalire; anthu okhala ndi mtendere nawe anakunyenga, nakuposa mphamvu; iwo akudya cakudya cako akuchera msampha pansi pako; mulibe nzeru mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Obadiya 1

Onani Obadiya 1:7 nkhani