Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nyimbo 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nkhunda yanga, wangwiro wangayu, ndiye mmodzi;Ndiye wobadwa yekha wa amace;Ndiye wosankhika wa wombala.Ana akazi anamuona, namucha wodala;Ngakhale akazi akulu a mfumu, ndi akazi ang'ono namtamanda.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 6

Onani Nyimbo 6:9 nkhani