Masaya ace akunga citipula cabzyalamo ndiwo,Ngati mitumbira yoyangapo masamba onunkhira:Milomo yace ikunga akakombo, pakukhapo madzi a nipa.