Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nyimbo 4:15-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Ndiwe kasupe wa m'minda,Citsime ca madzi amoyo,Ndi mitsinje yoyenda yocokera ku Lebano.

16. Galamuka, mphepo ya kumpoto iwe, nudze, mphepo iwe ya kumwela;Nuombe pamunda panga, kuti zonunkhiritsa zace ziturukemo.Bwenzi langa mnyamatayo, alowe m'munda mwace,Nadye zipatso zace zofunika.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 4