Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nyimbo 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, wakongola, bwenzi langa, namwaliwe, taona, wakongola;Maso ako akunga a nkhunda patseri pa cophimba cako:Tsitsi lako likunga gulu la mbuzi,Zooneka pa phiri la Gileadi.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 4

Onani Nyimbo 4:1 nkhani