Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nyimbo 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nditawapitirira pang'ono,Ndinampeza amene moyo wanca umkonda:Ndinamgwiriziza, osamfumbatula,Mpaka nditamlowetsa m'nyumba ya amai,Ngakhale m'cipinda ca wondibala.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 3

Onani Nyimbo 3:4 nkhani