Ngati sudziwa, mkaziwe woposa kukongola,Dzituruka kukalondola bande la gululo,Nukawete ana a mbuzi zako pambali pa mahema a abusa.