Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo panali amuna, anadetsedwa ndi mtembo wa munthu, ndipo sanakhoza kucita Paskha tsiku lomwelo; m'mwemo anafika pamaso pa Mose ndi pamaso pa Aroni tsiku lomwelo;

Werengani mutu wathunthu Numeri 9

Onani Numeri 9:6 nkhani