Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Alevi aike manja ao pa mitu ya ng'ombezo; pamenepo ukonze imodzi ikhale nsembe yaucimo, ndi inzace, nsembe yopsereza za Yehova, kucita cotetezera Alevi.

Werengani mutu wathunthu Numeri 8

Onani Numeri 8:12 nkhani