Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 7:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. cipande cimodzi cagolidi ca masekeli khumi, codzala ndi cofukiza;

21. ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwana wa nkhosa mmodzi wa caka cimodzi, zikhale nsembe yopsereza;

22. tonde mmodzi akhale nsembe yaucimo;

Werengani mutu wathunthu Numeri 7