Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 7:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

copereka cace ndico mbizi imodzi yasiliva, kulemera kwace ndiko masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi yasiliva ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwirizo zodzala ndi ufa wosalala wosanganiza ndi mafuta ukhale nsembeyaufa;

Werengani mutu wathunthu Numeri 7

Onani Numeri 7:13 nkhani