Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kuti tsiku lomwe Mose anatsiriza kumuutsa kacisi, namdzoza ndi kumpatula, ndi zipangizo zace zonse, ndi guwa la nsembe, ndi zipangizo zace zonse, nazidzoza ndi kuzipatula;

Werengani mutu wathunthu Numeri 7

Onani Numeri 7:1 nkhani