Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 6:26-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Yehova akweze nkhope yace pa iwe, nakupatse mtendere.

27. Potero aike dzina langa pa ana a Israyeli; ndipo ndidzawadalitsa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 6