Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 5:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atammwetsa madziwo, kudzatero, ngati wadetsedwa, nacita mosakhulupitika pa mwamuna wace, madzi odzetsa tembererowo adzalowa mwa iye nadzamwawira, nadzamtupitsa mbulu, ndi m'cuuno mwace mudzaonda; ndi mkaziyo adzakhala temberero pakati pa anthu a mtundu wace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 5

Onani Numeri 5:27 nkhani