Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 4:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nchito yonse ya ana a Agerisoni, kunena za akatundu ao ndi nchito zao zonse, ikhale monga adzanena Aroni ndi ana ace amuna; ndipo muwaike adikire akatundu ao onse.

Werengani mutu wathunthu Numeri 4

Onani Numeri 4:27 nkhani