Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 36:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Anakwatibwa mwa mabanja a ana a Manase mwana wa Yosefe; ndipo colowa cao dnakhala m'pfuko la banja la atate wao.

13. Awa ndi malamulo ndi maweruzo, amene Yehova analamulira ana a Israyeli ndi dzanja la Mose m'zidikha za Moabu pa Yordano ku Yeriko.

Werengani mutu wathunthu Numeri 36