Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 36:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuru a makolo a mabanja a ana a Gileadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, wa mabanja a ana a Yosefe, anayandikiza, nanena pamaso pa Mose, ndi pamaso pa akalonga, ndiwo akuru a makolo a ana a Israyeli;

Werengani mutu wathunthu Numeri 36

Onani Numeri 36:1 nkhani