Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 33:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mulandire dzikoli ndi kucita maere monga mwa mabanja anu; colowa cao cicurukire ocurukawo, colowa cao cicepere ocepawo; kumene maere amgwera munthu, kumeneko nkwace; mulandire colowa canu monga mwa mapfuko a makolo anu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 33

Onani Numeri 33:54 nkhani