Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 33:25-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Nacokera ku Harada, nayenda namanga m'Makeloti.

26. Nacokera ku Makeloti, nayenda namanga m'Tahata.

27. Nacokera ku Tahata, nayenda namanga m'Tara.

28. Nacokera ku Tara, nayenda namanga m'Mitika.

29. Nacokera ku Mitika, nayenda namanga m'Hasimona.

30. Nacokera ku Hasimona, nayenda namanga m'Moseroto.

Werengani mutu wathunthu Numeri 33