Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 33:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Nacokera ku Risa, nayenda namanga m'Kehelata.

23. Nacokera ku Kehelata, nayenda namanga m'phiri la Saferi.

24. Nacokera ku phiri la Saferi, nayenda namanga n'Harada.

Werengani mutu wathunthu Numeri 33