Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 33:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Maulendo a ana a Israyeli amene anaturuka m'dziko la Aigupto monga mwa makamu ao, ndi dzanja la Mose ndi Aroni, ndi awa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 33

Onani Numeri 33:1 nkhani