Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 32:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yairi mwana wa Manase anamka nalanda midzi yao, naicha Havoti Yairi. Ndipo Noba anamka nalanda Kenati, ndi miraga yace, naucha Noba, dzina lace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 32

Onani Numeri 32:41 nkhani