Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 32:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anawapatsa, ndiwo ana a Gadi, ndi ana a Rubeni ndi pfuko la hafu la Manase mwana wa Yosefe, dziko la Sihoni mfumu ya Aamori, ndi dziko la Ogi mfumu ya Basana, dzikoli ndi midzi yace m'malire mwao, ndiyo midzi ya dziko lozungulirako,

Werengani mutu wathunthu Numeri 32

Onani Numeri 32:33 nkhani