Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 32:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa iwo, Ngati ana a Gadi ndi ana a Rubeni aoloka nanu Yordano, yense wokonzekera ndi zankhondo pamaso pa Yehova, ndi dziko lagonjera inu; pamenepo muwapatse dziko la Gileadi likhale lao lao;

Werengani mutu wathunthu Numeri 32

Onani Numeri 32:29 nkhani