Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 32:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anapsa mtima pa Israyeli, nawayendetsa-yendetsa m'cipululu zaka makumi anai, kufikira utatha mbadwo wonsewo udacita coipa pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Numeri 32

Onani Numeri 32:13 nkhani