Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 31:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo golidi yense wa nsembe yokweza ya Yehova amene anapereka kwa Yehova, wofuma kwa atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, ndiwo masekeli zikwi khumi ndi zisanu ndi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 31

Onani Numeri 31:52 nkhani