Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 31:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tabwera naco copereka ca Yehova, yense cimene anacipeza, zokometsera zagolidi, unyolo, zikwinjiri, mphete zosindikizira, nsapule, ndi mkanda, kucita cotetezera moyo wathu pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Numeri 31

Onani Numeri 31:50 nkhani