Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 31:42-44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

42. Ndipo kunena za gawo la ana a Israyeli, limene Mose adalicotsa kwa anthu ocita nkhondowo,

43. (ndipo gawo la khamulo ndilo nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu,

44. ndi ng'ombe zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi cimodzi,

Werengani mutu wathunthu Numeri 31