Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 31:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo usonkhetse anthu ankhondo akuturuka kunkhondo apereke kwa Yehova; munthu mmodzi mwa anthu mazana asanu, mwa ng'ombe, mwa aburu, mwa nkhosa ndi mbuzi, momwemo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 31

Onani Numeri 31:28 nkhani