Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 30:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kama mwamuna wace akamletsa tsiku lakumva iye; pamenepo adzafafaniza cowinda cace anali naco, ndi zonena zopanda pace za milomo yace, zimene anamanga nazo moyo wace; ndipo Yehova adzamkhululukira.

Werengani mutu wathunthu Numeri 30

Onani Numeri 30:8 nkhani