Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 30:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akacitira Yehovacowinda, kapena akalumbira lumbiro ndi kumangira moyo wace codziletsa, asaipse mau ace; azicita monga mwa zonse zoturuka m'kamwa mwace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 30

Onani Numeri 30:2 nkhani