Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 30:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mwamuna wace akakhala naye cete tsiku ndi tsiku; pamenepo akhazikira zowinda zace zonse, kapena zodziletsa zace zonse, ziri pa iye; wazikhazikitsa, popeza anakhala naye cete tsikuli anazimva iye.

Werengani mutu wathunthu Numeri 30

Onani Numeri 30:14 nkhani