Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 30:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati mwamuna wace anazifafanizadi tsiku lakuzimva iye, zonse zoturuka m'milomo yace kunena za zowinda zace, kapena za codziletsa ca moyo wace sizidzakhazikika; mwamuna wace anazifafaniza; ndipo Yehova adzamkhululukira Iye.

Werengani mutu wathunthu Numeri 30

Onani Numeri 30:12 nkhani