Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 3:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amuna onse oyamba kubadwa, powerenga maina, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri mphambu atatu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 3

Onani Numeri 3:43 nkhani