Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 3:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo coyang'anira iwo, udikiro wao wa ana a Merari ndiwo matabwa a kacisi, ndi mitanda yace, ndi mizati ndi nsanamira zace, ndi makamwa ace, ndi zipangizo zace zonse, ndi nchito zace zonse;

Werengani mutu wathunthu Numeri 3

Onani Numeri 3:36 nkhani