Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ana oyamba onse ndi anga; tsiku lija ndinakantha ana oyamba onse m'dziko la Aigupto ndinadzipatulira ana oyamba onse m'Israyeli, kuyambira munthu kufikira coweta; ndiwo anga; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Numeri 3

Onani Numeri 3:13 nkhani