Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 29:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Izi muzikonzera Yehova mu nyengo zanu zoikika, pamodzi ndi zowinda zanu, ndi zopereka zanu zaufuru, za nsembe zanu zopsereza, ndi za nsembe zanu zaufa, ndi za nsembe zanu zothira, ndi za nsembe zanu zoyamika.

Werengani mutu wathunthu Numeri 29

Onani Numeri 29:39 nkhani