Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 29:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku laciwiri muzibwera nazo ng'ombe zamphongo khumi ndi ziwiri, nkhosa zamphongo ziwiri, ana a nkhosa khumi ndi anai a caka cimodzi, opanda cirema;

Werengani mutu wathunthu Numeri 29

Onani Numeri 29:17 nkhani