Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 29:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwezi wacisanu ndi ciwiri, tsiku loyamba la mweziwo, muzikhala nako kusonkhana kopatulika; musamacita nchito ya masiku ena; likukhalireni inu tsiku lakuliza malipenga.

Werengani mutu wathunthu Numeri 29

Onani Numeri 29:1 nkhani