Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 28:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo unene nao, Nsembe yamoto imene muzibwera nayo kwa Yehova ndiyi: ana a nkhosa awiri a caka cimodzi opanda cirema, tsiku ndi tsiku, nsembe yamoto yosalekeza.

Werengani mutu wathunthu Numeri 28

Onani Numeri 28:3 nkhani