Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 28:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nsembe zace zothira ndizo: limodzi la magawo khumi la bini wa vinyo ndiwo wa ng'ombe imodzi, ndi limodzi la magawo atatu la hini likhale la nkhosa yamphongo, ndi limodzi la magawo anai a hini likhale la mwana wa nkhosa; ndiyo nsembe yopsereza ya mwezi uli wonse kunena miyezi yonse ya caka.

Werengani mutu wathunthu Numeri 28

Onani Numeri 28:14 nkhani