Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 28:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo poyamba miyezi yanu muzibwera nayo nsembe yopsereza ya Yehova: ng'ombe zamphongo ziwiri, ndi nkhosa yamphongo imodzi, ndi ana a nkhosa asanu ndi awiri a caka cimodzi opanda cirema;

Werengani mutu wathunthu Numeri 28

Onani Numeri 28:11 nkhani