Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 27:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo aime pamaso pa Eleazara wansembe, amene amfunsire monga mwa ciweruzo ca Urimu pamaso pa Yehova; ponena iye azituruka, ndi ponena iye azilowa, ndi iye ndi ana onse a Israyeli pamodzi naye, ndiwo khamu lonse.

Werengani mutu wathunthu Numeri 27

Onani Numeri 27:21 nkhani