Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 27:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza munapikisana nao mau anga m'cipululu ca Zini, potsutsana nane khamulo, osandipatula Ine pa madziwo pamaso pao. Ndiwo madzi a Meriba m'Kadesi, m'cipululu ca Zini.

Werengani mutu wathunthu Numeri 27

Onani Numeri 27:14 nkhani