Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 27:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anayandikiza ana akazi a Tselofekadi mwana wa Heferi, ndiye mwana wa Gileadi, ndiye mwana wa Makiri, ndiye mwana wamwamuna wa Manase, wa mabanja a Manase mwana wa Yosefe; ndipo maina a ana ace akazi ndiwo, Mala, Nowa, Hogila ndi Milika ndi Tiriza.

Werengani mutu wathunthu Numeri 27

Onani Numeri 27:1 nkhani