Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:65 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Yehova adanena za iwowa, Adzafatu m'cipululu. Ndipo sanatsalira mmodzi wa iwowa koma Kalebi mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:65 nkhani